Zikomo Yesu – by The QFM
M'malo moti tizinyinyirika ndi mauthenga a kukonzanso (Reform Messages), bwanji tiyambe kumuthokoza Mulungu wathu kaamba ka mphatso yapaderadera ngati imeneyiyi, imene siinaperekedwe kwa wina aliyense pa dziko lino, koma kwa ife tokha basi!... Ndi zomvetsa chisoni kuti ambiri mmalo molandira ndi mtima wonse mauthenga okonzanso-wa, timanyalanyaza (monga ana a Israel) ndi kumuonetsa Mulungu ngati opanda nzeru potiuza zoyenera anthu Ake kuchita... komano tikanadziwa chikondi ndi ma plan a Mulungu wathu wachifundoyo — pa ife ana Ake, bwenzi tikungonena kuti "Zikomo Yesu" pa zinthu zonse zomwe Akutichitira, podziwa kuti Akuchita zonse ku ubwino wathu!

▶︎
Takachengetedzewa Zvizere

▶︎
Usikate Tamaa- Powerful Swahili worship song

▶︎
Ndionetseni – by The QFM

▶︎
Lalikira Mau – by The QFM

▶︎
USINIACHE BWANA 😭💔 | This Worship Will Touch Your Heart

▶︎
SDA HYMN MASHUP by Hope in Christ Singers Official Video #The Lord is coming concert Edition 2

▶︎
Lombo Lithu – by The QFM

▶︎
Reka ndate Imana Data | Josh Ishimwe (Gakondo Style)

▶︎
Salama ROHONI | Deep Soaking Worship | Swahili Hymn | By the Worshippers' Altar.

▶︎
New Apostolic Church (Malawi) - Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

▶︎
Mau Ofatsa – by The QFM

▶︎
HAPPY SABBATH - Christ in Hymns Sing-Along with JEHOVAH SHALOM ACAPELLA | 2025

▶︎
Tili ndi iwe – by The QFM

▶︎
Mundichotsere – by The QFM
![[Live Praise and Worship Shabbat] by Jehovah Shalom Acapella | Christ in Hymns Episode 10](https://i.ytimg.com/vi/Fjt2qYe06jM/hqdefault.jpg?sqp=-oaymwEjCNACELwBSFryq4qpAxUIARUAAAAAGAElAADIQj0AgKJDeAE=&rs=AOn4CLAQsPEhs5TsMxrMJsRsvgF4EYUn8w)
▶︎
[Live Praise and Worship Shabbat] by Jehovah Shalom Acapella | Christ in Hymns Episode 10

▶︎
Kristo Wa Neema Yote Imbisha Moyo Wangu

▶︎
Kaamba ka Nyimbo by The QFM

▶︎
Shimwa Yesu wanjye - James&Daniella(lyrics)

▶︎
