Mimba ya Mayi Chrissy Chembe ikungofufuma ngati oyembekezera koma alibe pakati

Mimba ya Mayi Chrissy Chembe ikungofufuma ngati ndi oyembekezera koma ali matenda. mwana wao komanso wa abale awo akhonzera Ku CDSS koma akulephera kupita, 3 weeks tsopano