Mayi Wina Watopa ndikugonana ndi Ndondocha
Mverani program ya Zilipati yokhudza nkhani ya mayi wina ku Blantyre yemwe akuulura kuti watopa ndikusamalira ndondocha zomwe mamuna wake anakatenga kwa sing'anga wina ku Mozambique kuti alemere. Mwa zina mayi-yu wauza Zilipati kuti amauzidwa kuti azigonana ndi ndondocha yaimuna ndipo mamuna wake azigonana ndi ndondocha yaikazi Iye wauzaso Zilipati kuti anauzidwa kuti aphe mwana wawo mmodzi komanso adzipha wachibale chaka chilichonse. Programuyi inagulitsidwa pa #MIJ FM pa program ya #zilipati, ife a Mvangeli Online tiilibe umwini pa video imeyi.

▶︎
Zilipati: Kulira Kwa Atsikana omwe ali m'dziko La Oman

▶︎
Zozoopsa! Munthu Amwalira Kawiri!

▶︎
Times Investigation on Grave Robberies – January 21, 2024

▶︎
Chipoko Nellie, Muzionetsetsa 3, Movie

▶︎
Umboni wa Mayi Mawindo - za Gahena ndi Paradaizo

▶︎
Omwalira apezeka wa moyo

▶︎
TIPANGE DAWA SAID ZAMBIA

▶︎
KWATULUKA AUDIO YA KUNKUYU AKUYANKHULA ZA IMFA YA CHILIMA| NAMIWA SIBASI WAPHA MCP| MALAWI NEWS

▶︎
MFUMUKAZI FOR 11 DECEMBER 2025

▶︎
Janet ulendo waphedwa ndi poison waku ufiti

▶︎
Zoopsa! Mneneli akanataya moyo atasala chakudya masiku ochuluka...

▶︎
ANTHU AKUYIPHULA UKU. TAMVANI IZI PA PROGRAM YA ZILIPATI KUWULULA.

▶︎
CHUMA WACHIPEZA KWA NSING'ANGA KU PHALOMBE KOMA AKUONA ZOOPSYA

▶︎
MDYANGU COMEDY SERIES | 13 DECEMBER 2024

▶︎
NKHANI YA MAYI YEMWE ANABEREDWA ANA AKE ONSE! ZOOPSATU

▶︎
DAUDI SULEMAN AMUKHAULITSA NDI MAFUNSO LERO NGATI ZILI ZOONA PAZOFUNA KUGULA MACHINE A 3 BILLION

▶︎
Kangaude: Apolisi anawombela Galimoto ya Andrew Banda kamba koti inanyamula ma Somalians

▶︎
Msika Wa Ziwalo part 2...

▶︎
Simandou | SimFer KIBARO EP1

▶︎
