Ndikhulupilira Bible (Official Video) — Area 47 Senior Youth Choir
Words & Music: Ndudirim Nwachukwu Accessed from: Tunefulness.scores Title: Oh yes, I believe @tunefulness.scores _________________________________________ Chichewa Lyrics: 1. Ndikhulupilira Bible, Ndukhulupilira Yesu, Kuti anafa pamtanda kufera 'ne. Ndikhulupirira Tate, Mwana ndi Mzimu Oyera, Ine, ine, ndikhulupira. Chorus Kuti anandiferane, Kuti ndikhale ndi moyo. Anafa, anafa, anafa kufera ine, Akufuna ndisiye tchimo, anafa pamtanda paja, Nagwazidwa Mbuye wanga. 2. Ndikhulupilira Yesu, Abweradi posachedwa, Kudzatenga onse kunka nawo mwamba. Kuti tikhale ndi moyo, Osatha mudziko ilo, Ine ine ndikhulupira.

▶︎
Pofika Kumapeto (Official Video) — Area 47 Senior Youth Choir

▶︎
Greatest SDA Hymns Vol.7 | Sabbath Songs for Prayer, Rest & Reflection

▶︎
Area 49 SDA Youth Choir OkongolaFilm by Will

▶︎
Christ in Song 15 Hymns Vol 1 SDA Songs SDA Hymns ||Christ In Song

▶︎
The Gentiles Ndine Mfulu (Official Video)

▶︎
Oh yes! I believe

▶︎
Malawi Tembenuka (Official Video) — Area 47 Senior Youth Choir & CMC Mass Choir

▶︎
Ubuntu Voices | Voices of Peace | African Gospel Worship to the Prince of Peace

▶︎
The Chronicles Lilongwe Band-Thandizo Langa

▶︎
24/7 HYMNS LIVESTREAM | Best Christian Hymns Compilation | Old & Traditional Church Songs

▶︎
Kasemba Future Adventist Men - M'mava Motani (Official Music Video)

▶︎
Chiuzimbi_SDA_Senior_Youth_Choir_Tsogolani_Yehova

▶︎
MALAWI SDA CAPELLA PART 2 - DJ Chizzariana

▶︎
Ndikonda M'lungu Wanga (Official Video) — Area 47 Senior Youth Choir

▶︎
Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

▶︎
Seventh Day Adventist (SDA) Music Collection - Zambia

▶︎
Voices of Hope | African Worship Choir | A Song of Faith, Light and Restoration

▶︎
Yehova Ndinu Chikopa (Official Video) — Area 47 Senior Youth Choir

▶︎
