After Tombstone Unveiling - MBUMBA KUGWILA #KALONGA SOSOLA IX 23 08 2025 Evening -Madzulo Ake
Pa 23 August 2025. Kenaka pambuyo pa mwambo wa chirizachi madzulo ake kudabwera Mbumba za mtsogoleri wa Chifukwato cha Achewa ndi kutidziwitsa kuti iwo adapeza ndi kugwira mfumu ina yolowa m'malo mwa Kalonga Sosola #8. Izi zidaoneka ngati kutulo kwa mafumu onse ndi atsogoleri a Chifukwato amene adaali akadalipo pa usikuwo. Mwachimwene ntchembere gandule, ntchembere mbaye, Makewana ndi anankungwi onse adadumpha nagwira wa pampando wa Chifukwato Cha Achewa amenenso ndi wakubanja kwao kukhala mlowam'malo mwa Kalonga Sosola #8. Uku kudaali kutha kwa siwa yomwe idawatengera zaka 162 chifereni cha Kalonga Sosola #8, Tonse tidadzazidwa ndi Chimwemwe chodzadza tsaya pamene banjali lidatibweretsera mthunzi ngati achewa tonse muno m'Malawi. Motero ndinenetse pano kuti Kuyambira pa 23 August 2025 achewa Ngati mtundu tiri ndi mfumu ya mfumu Kalonga #9 mom'muno m'Malawi. Uku ndi Mankhamba ku Chikwawa cha boma la Salima. Potsatira kusamkhidwa kwa wapampando wa Chifukwato cha Achewa kukhala Kalonga Sosola #9 Ndiye kuti nthawi yomweyo Kalonga Sosola saalinso mtsogoleri wa Chifukwato. Iye angokhala mlangazi wamkulu. Chewa people were primarily originated from Luba area in the Democratic Republic of Congo formerly called ' Zaire'. They moved into Zambia and in the high hills of Malawi.Few were scattered in Mozambique and Zimbabwe. According to history and other narratives,they are two major clan of Chewa people called Banda and Phiri. In Malawi the last Kalonga Sosola #8 was believed to be slained by Yao some years back in the area called ' Makhamba' Dedza district. On 23 August ,the culture grouping, Malawi Chewa Heritage fondly called' chifukwato Cha Chewa ' organized the memorial event where the tombstone of Kalonga Sosola #8 was unvailed. The event was attended by different senior chiefs from Malawi and people from all of walks of life who gathered at Makhamba in Dedza district. During the event, chiefs conducted the libation in honour of the spirits of kalonga sosola #8 and immediately after the traditional ceremony,kalonga sosola from T/ A Khombedza in Salima assumed the tittle' Kalonga Sosola #9 who is now a king for Chewa people in Malawi.Kalonga Sosola #9 comes from Phiri clan. In his recent key note addresses, Kalonga Sosola #9 has been preaching about unity and love among Chewa people and hardworking to bring fortunes. The inauguration ceremony of Kalonga Sosola #9 will take place in Chikwawa, Salima district on 1 November this year. The event will be spiced up by different traditional dances such as Gulewankulu, Chisamba, M' ganda, Chintali to name but afew. Lovemore katanda _ chifukwato Cha achewa#

His Majesty Kalonga Sosola IX on his relationship with LUNDU, GAWA UNDI Kulamba and Mkaika. #Sosola

Mwana wechipiri haasi wako

MY DAUGHTER WON I ENROLLED HER BACK TO SCHOOL

His Majesty Kalonga Sosola IX News Flash with Snr Chief Dr Kaomba Refuting Fake News 06 05 2026 #ix

Gutu: Akabhadhara Kubvisa Mwana Wangu Brugwa Kwete Kuti Akandipa Pfuma

Unveiling 23/08/2025 - HONOURING THE KING OF THE MARAVI (MALAWI): THE LEGACY OF KALONGA SOSOLA VIII.

91 Year-Old Grandmother Living Alone In A Mountain Village Forgotten By The World

NO ONE Understood What Was Happening... Then They Started LAUGHING And It All Made Sense!

Sunday service preaching Pastor P.Ekundayo

TOP EXTREME SURVIVAL CHALLENGE IN HEAVY RAINSTORM ON RAFT CATCH & COOK WITH MY DOG RELAXING 4K ASMR!

Photographers Who Became Friends With Wildlife in the Sweetest Way! 😍🐾

Kalonga Sosola IX Pa Dambule 2026 Mnjedza Gule Wa Nkulu @ Mankhamba City -#Burial Site #cleanupday

Wedza - Panorohwa Munhu Nhasi Pano. Hauise Dombo paGuva raBaba, Hausi Mwana wemuMusha Iwe. (Part 1)

The Assassination of Herbert Chitepo: His Life and Political Journey

JARIYA TALKS ABOUT HER LOVE FOR DALIENS 30 YEARS AFTER HIS DEATH ,,,,,,

80 Scariest Tourist Attractions In The World

#Kalonga Sosola IX Press Briefing @ #Mankhamba HQ 15 07 2026 #zodiak2026 #Times360Malawi #Mibawa

HOTUBA YA MAREMU CHRIS MSANI WA NYARUGUSU HIZI HAPA SABABU ZA KIFO CHAKE

ISSUE NANAMAN KAY CARLA | HANO BAYAN!

