Deadly Feud: Kamuzu Banda vs Samora Machel

Zinthu zambiri zimakambidwa pa nkhani ya imfa ya Samora Machel, video yi ikufotokoza zifukwa zimene zidapangitsa udani pakati pa Kamuzu Banda ndi Samora Machel wa ku Mozambique