DRIEMO COMPENSATION (Lyrics video)
Intro Kuti mwina compensation Driemo Ndidzapereke moyo wanga Verse1 Oh mtima uwupereke, kwaine ndiwutenge Don't you worry about safety Ndidzachengetera chengetera chengetera I know mtima unaswekapo You've been there unalirapo, ululu mumtima kufikapo Ukaganizira ganizira ganizira Paiwe ndilola ndipepere, chikondi chisaperewere Olo pa ground paterere I will love you the same baby Hook Oh udzandifunse Ndikadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga x2 Verse2 Don't be scared to love me more Zakale zapita it's me and you Undiuze pomwe Pali mantha ako I know mtima umakana ukandiunika Umaona ngati Aja anakunamiza koma I wanna be your soldier Your fighter Protector Defender I just wanna be your friend for life Hook Oh udzandifunse Ndikadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga x2 Bridge Ooh udzandifunse Udzandifunse, mwina compensation ndidzapereke moyo wanga eeee Hook Oh udzandifunse Ndikadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga x2 Tags COMPENSATION, DRIEMO, VAN NGONGO, VJ KEN, RON CZ, 8MEDIA #DRIEMO #compensation #LYRICOZMmuziq

Driemo - Loyalty (Mzaliwa Album) Lyrics

Driemo - pano || lyrics

The Richest Family in ZIMBABWE & The Secrets Behind Their Fortune...

Like You | Tatiana Manaois (OFFICIAL MUSIC VIDEO)

driemo mtendere prod by tactic fat_nyanda (oficial video_FAY-BOY)
![Kell Kay - Bana Pwanya [Feat. Yo Maps & Prince Luv] ( Official Music Video)](https://i.ytimg.com/vi/7htEtgbGaw4/hqdefault.jpg?sqp=-oaymwEjCNACELwBSFryq4qpAxUIARUAAAAAGAElAADIQj0AgKJDeAE=&rs=AOn4CLCTsF-vuytw2-f8WP6tv9tg7MoutQ)
Kell Kay - Bana Pwanya [Feat. Yo Maps & Prince Luv] ( Official Music Video)

Chillmaster Music Mixtape (Zim Music 2024) Mixed By DJ Stanza MrMajestic

Driemo - No Insurance (Lyrics)

Driemo - Popo (Lyrics) Somebody call the police i beg

LOCKO SAWA ROMANCE OFFICIAL VIDEO

Driemo – Joker (Official Music Video)

DRIEMO MAWA LYRICS

Driemo- Insurance (Lyrics)

RJ Kanierra - TIA (Official Video)

Helplessly Tatiana Manaois - Lyrics Video

Driemo_Imagine ft Xaven (Mzaliwa album) Lyrics

Driemo - Magini (Lyric Video)

Driemo magician mixtape 2025 songs

KB Ft Chewe & Triple M - Kalema (Official Music Video)

