Lloyd Phiri Star of the Week Interview

Star of the week ya sabata inu Henry Kasowa akucheza ndi Lloyd Phiri pamene akufotokozapo Zinthu zina zimene zimapangitsa kuti athu Oyimba amene anayamba kuyimba pakanthawi azione ngati salimbika pa luso lawo kusiyana ndi amene anayamba Kunyimba kumene.