Kwathu Kwamuyaya, Amayi Athu | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
Kodi ndi Phunziro Lofunika Kwambiri Liti Limene Mulungu Anaphunzitsa Anthu Kudzera mu Moyo wa Nsomba za Salimoni? Nsomba za salimoni zimakhala m’nyanja kenako zimabwerera komwe zinabadwira kuti zikabereke. M’njira imeneyi, monga momwe nsomba za salimoni zimapirira ululu pogwiritsa ntchito mphamvu zake zosungidwa popanda kudya, ifenso tiyenera kugonjetsa ululu wa kubadwa mwatsopano mwa kusiya zizolowezi zonse zoipa ndi makhalidwe omwe taphunzira m’dziko lino ndikuyesetsa kubwerera kumudzi kwathu kwamuyaya kumwamba komwe Atate ndi Amai amakhala. Mamembala a Mpingo wa Mulungu Amachita “Mawu a Chikondi cha Amayi” Padziko Lons. Pa nthawi ino, pamene mitundu yonse ikuuluka kupita m’manja mwa Amai Akumwamba a Yerusalemu monga momwe Baibulo linaneneratu, mamembala a Mpingo wa Mulungu nthawi zonse amachita “Mawu a Chikondi cha Amayi” motsatira ziphunzitso Zawo, kuwulula ulemerero wa Amai Akumwamba Yerusalemu ku dziko lonse lapansi kudzera mu ntchito zawo zabwino. Ndipo musafanizidwe ndi makhalidwe a pansi pano: koma mukhale osandulika, mwa kukonzanso kwa mtima wanu, kuti mukazindikire chimene chili chifuno cha Mulungu, chabwino, ndi chokondweretsa, ndi changwiro. Aroma 12:2 Nyamuka, wala, pakuti kuunika kwako kwafika, ndi ulemerero wa Yehova wakutulukira. Pakuti taona, mdima udzaphimba dziko lapansi, ndi mdima wa bii mitundu ya anthu; koma Yehova adzakutulukira ndi ulemerero wake udzaoneka pa iwe. Ndipo amitundu adzafika kwa kuunika kwako, ndi mafumu kwa kuyera kwa kutuluka kwako. Yesaya 60:1–3 [Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.] 〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org 〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny 〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com

Kulimbikitsidwa kwa Kirusi ndi Tsogolo Lathu | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu

Chikhulupiriro cha Yudasi Isikariote | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu

Keebkwm Txuj Moo Zoo Tuaj Txug XeesKhuam | Nruag Hawj

Rural Girl Becomes Infertile CEO’s Miracle—One Night, She’s Pregnant with Triplets! Spoiled Rotten!

Con el amor de una madre, hagamos del mundo un lugar donde todos sean felices y nadie sea descuidado

Best Christian Worship Songs 2026 ✝️ Nonstop Christian Praise & Worship Music | Feel God's Presence

Ny Aingam-Panahin'i Kyrosy sy ny Hoavintsika | FAFIMT

Fatty Liver Expert: The Toxic Ingredient Silently Filling Your Liver With Fat - Dr David Unwin

Bhaibheri neMhuri Yokudenga | Kereke yaMwari

El amor viene de Dios | IDDSMM, Iglesia de Dios

Omahala gIiponga nOmahala gOmayambeko. | Egongalo lyaKalunga

Biblia na Familia ya Mbinguni | Jmdklm, Kanisa la Mungu

눈물의 역사 - 효정찬양 | CSWB

Professor Jiang: World War 3 Is About To Begin, Let Me Explain!

Paska ndiye njira ndi Choonadi | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu

Charlie Kirk’s FINAL Debate with Cliffe Knechtle… The Moment Everyone Talks About! 🤯

Greatest SDA Hymns for Prayer & Peace | Adventist Worship | Peaceful Adventist Music

Waanti Haaraan Siif Ta'a! Luba/Professor Gammachiis Dastaa

Ang Pananampalataya ni Judas Iscariote | Church of God

