Ulemerero wa Ufumu wa Kumwamba | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
Palibe Munthu Angayeze Zimene Mulungu Wakonzera Ana Ake Mtumwi Paulo anakhala mneneri wamkulu chifukwa adaona ulemerero wa kumwamba kwachitatu. M’chilengedwe chonse chachikulu chimene anthu sangathe kuchimvetsa, Mulungu watikonzera tsogolo laulemerero. Ichi ndichifukwa chake watiitana kuti tikhale ndi kawonedwe kokulirapo, kuti tisayang’ane dziko lapansi, koma chilengedwe chonse—ndiko, ku ufumu wa kumwamba. Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai Anabwera Kudzatsegula Maso Athu Kuti Tione Ufumu wa Kumwamba Tiyenera kugonjetsa mavuto a lero poyang’ana pa ulemerero wa ufumu wa kumwamba ndi tsogolo lowala limene likutiyembekezera kumeneko. Ngati tilephera kukhulupirira ufumu wa kumwamba, pamapeto ake tidzataya chikhulupiriro chathu pakati pa kuvutika kwakanthawi ndikusiya choonadi. Komabe, ngati timvetsetsa zenizeni za ufumu wa kumwamba, chikhulupiriro chathu chidzakula tsiku ndi tsiku, kutithandiza kutenga nawo mbali mu ulemerero wake. pakuti chisamaliro cha thupi ndi imfa; koma chisamaliro cha mzimu ndi moyo ndi mtendere. Aroma 8:6 Pakuti ife tinapulumutsidwa ndi chiyembekezo; koma chiyembekezo chimene chioneka si chili chiyembekezo ai; pakuti ayembekezera ndani chimene achipenya? Koma ngati tiyembekezera chimene sitichipenya, pomwepo tichilindirira ndi chipiriro. Aroma 8:24–25 [Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.] 〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org 〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny 〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com

Paska ndiye njira ndi Choonadi | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu

Eadhimo lyOshilongo shEgulu | Egongalo lyaKalunga

Pentecôte // Ap. Dieudonné Nahimana

Deported To Nigeria With British Kids- SHOCKING STORY!

Eitaalo lyaJudas Iskariot | Egongalo lyaKalunga

I Was Captured and Faced Execution by ISIS — How God Sent Angels to Save Me? | Traore Testimony

ELIZABETH MOKORO AMUA KUSEMA UKWELI NOMINAL SDA NA KUWAAMBIA WATOKE GC ISHAPOTOKA

الغَنِيُّ وَلِعَازَرُ | كنيسة الله، آن سانغ هونغ، الله الأم

President Ruto's Speech During a Church Service at the Seventh-day Adventist Church,Kajiado County

La gloria del reino de los cielos | Iglesia de Dios Sociedad Misionera Mundial

Are Seventh-day Adventists Actually Christian? What Do SDAs Believe?

GLOBAL MIDNIGHT PRAYERS 16TH JUNE 2026 | JOSHUA GENERATION

Românii care schimbă vieți în Africa: construiesc școli și transformă comunități

Why My husband had a spiritual wife|The man turned into a snake & what followed will shock you

Injili Iliyoongozwa na Mungu | Jmdklm, Kanisa la Mungu

🌟 Say This 3 Times — God Will Open Doors You Never Expected || Kathryn Kuhlman

ಮನುಷ್ಯರು ಮಾಡಲಾಗದ ಕಾರ್ಯ | ಚರ್ಚ್ ಆಫ್ ಗಾಡ್

Fit für die Zukunft: Jesus Christus bereitet seine Leute vor (Joh 13–17) | Hartmut Jaeger

A Message Worth Sharing

