Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luka 10-13: Yesu atuma anthu 72-Yesu aphunzitsa za kupemphera

Luka full movie:    • Chichewa full movie: Moyo wa Yesu Khristu ...   - Luka 1-2:    • Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luk...   ; Luka 3-6:    • Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luk...   , Luka 7-9:    • Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luk...   , Luka 10-13:    • Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luk...   , Luka 14-21:    • Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luk...   , Luka 22-24:    • Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luk...   , - Moyo wa Yesu Khristu | YOHANE | momwe mungalandirire moyo wosatha ndi Mulungu:    • Chichewa full movie: Moyo wa Yesu Khristu ...   - Chichewa | Machitidwe a Atumwi | Pambuyo pa kuukitsidwa kwa Yesu: Mzimu Woyera ukugwira ntchito | Acts Full movie:    • Chichewa | Machitidwe a Atumwi | Pambuyo p...   - Chichewa full movie: Moyo wa Yesu Khristu | MATEYU | momwe mungalandirire moyo wosatha ndi Mulungu:    • Chichewa full movie: Moyo wa Yesu Khristu ...   -- Playlist christian's movie in Chichewa:   • Chichewa christian's movies   - CHICHEWA - Gospel of Matthew:    • CHICHEWA - Gospel of Matthew   - CHICHEWA - Gospel of John:    • CHICHEWA - Gospel of John   - CHICHEWA - Gospel of Luke    • CHICHEWA - Gospel of Luke   - CHICHEWA - Gospel of Mark:    • CHICHEWA - Gospel of Mark   - Jesus film: https://www.jesusfilm.org/watch/jesus... - Read and listen to the bible in your language: https://www.bible.com/it/bible/1708/J... - The Gospel of John in English :    • The Gospel of John | Full Movie | Christop...   - Acts of the Apostles in English:    • Acts Of The Apostles (1994) | Full Movie |...   - The Gospel According to Matthew:    • The Gospel According to Matthew | Full Mov...   11 - LUKA Mau Oyamba Buku la Luka likunena za Yesu monga Mpulumutsi wolonjezedwa uja wa Aisraele komanso Mpulumutsi wa anthu onse. Luka akunena kuti Yesu anaitanidwa ndi Mzimu wa Ambuye kuti, “awuze anthu osauka Uthenga Wabwino” (4.18), ndipo uthengawo ukuonetsa kuti Yesu anali wokhudzidwa ndi anthu amene ali ndi zosowa zosiyanasiyana. Nkhani inanso imene ikuonekera kwambiri mu buku la Luka ndiyo ya chimwemwe. Makamaka izi zikupezeka mu mitu yoyambirira ya bukuli pamene akunena za kubwera kwa Yesu, komanso kumapeto pamene Yesu akukwera kunka kumwamba. Luka analembanso mbiri ya chiyambi ndi kukula kwa mpingo wa Chikhristu Yesu atakwera mu buku lija la Machitidwe. Bukuli lili ndi magawo awiri (mutu 1—2 ndi 9—19) m'mene muli nkhani zimene zikupezeka mu Luka yekha, nkhanizi ndi monga nyimbo ya angelo ndi ulendo wa abusa kukaona Yesu ali kakhanda, mwana Yesu ali m'Kachisi, ndiponso fanizo la Msamariya wachifundo ndi la Mwana wolowerera. Mu buku lonseli, nkhani yaikulu yagona pa pemphero, Mzimu Woyera, udindo wa azimai pa utumiki wa Yesu komanso kuti Mulungu amakhululukira machimo. Za mkatimu Mau oyamba 1.1-4 Kubadwa ndi ubwana wa Yohane Mbatizi komanso Yesu 1.5—2.52 Utumiki wa Yohane Mbatizi 3.1-20 Ubatizo ndi kuyesedwa kwa Yesu 3.21—4.13 Utumiki wa Yesu ku Galileya 4.14—9.50 Kuchokera ku Galileya kupita ku Yerusalemu 9.51—19.27 Sabata yomaliza mu Yerusalemu ndi madera oyandikira 19.28—23.56 Kuukanso, kuonekera ndi kukwera kumwamba kwa Ambuye 24.1-53 - Movies with subtitles: The gospel of John - more than 2200 subtitles. Full movie: Languages starting with : A :    • The gospel of John: the life of Jesus | fu...   B :    • The gospel of John: the life of Jesus | fu...   C :    • The gospel of John: the life of Jesus | fu...   D - E - F:    • The gospel of John: the life of Jesus | 17...   G - H:    • The gospel of John: the life of Jesus | 20...   I - J :    • The gospel of John: the life of Jesus | 11...   K :    • The gospel of John: the life of Jesus | 31...   L :    • The gospel of John: the life of Jesus | 11...   M:    • The gospel of John: the life of Jesus | 31...   N :    • The gospel of John: the life of Jesus | 18...   O - P - Q - R :    • The gospel of John: the life of Jesus | 24...   S :    • The gospel of John: the life of Jesus | 22...   T :   • The gospel of John: the life of Jesus | 24...   U - V - W - Y - Z:    • The gospel of John: the life of Jesus | 25...   Acts of apostles, - A and B:    • Acts of the apostles | After the resurrect...   C and D:    • Acts of the apostles | After the resurrect...   E to H:    • Acts of the apostles | After the resurrect...   I -J K:    • Acts of the apostles | After the resurrect...   L - M :    • Acts of the apostles | After the resurrect...   N O P:    • Acts of the apostles | After the resurrect...   Q -R -S:    • Acts of the apostles | After the resurrect...   T - U :    • Acts of the apostles | After the resurrect...   V-W-Y-Z:    • Acts of the apostles | After the resurrect...   - The gospel of Matthew -- A:    • The gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , B:    • The gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , C:    • The gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , D-E-F:    • Gospel of Matthew | Jesus Christ: from bir...   , G-H:    • Gospel of Matthew | Jesus Christ: from bir...   , I-J-L:    • Gospel of Matthew | Jesus Christ: from bir...   , K:    • The Gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , M:    • The Gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , N:    • The Gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , O-P-Q-R:    • Gospel of Matthew | Jesus Christ:from birt...   , S:    • The Gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , T:    • The Gospel of Matthew | Jesus Christ: from...   , U-V-W-Y-X-Z:   • Gospel of Matthew | Jesus Christ: from bir...  

Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luka 14-21: Fanizo la mwana wotayika - Za mavuto ndi mazunzo
▶︎

Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luka 14-21: Fanizo la mwana wotayika - Za mavuto ndi mazunzo

Chichewa | Machitidwe a Atumwi | NTC.20-28:Uthenga wabwino unayamba kufalikira padziko lonse lapansi
▶︎

Chichewa | Machitidwe a Atumwi | NTC.20-28:Uthenga wabwino unayamba kufalikira padziko lonse lapansi

OLUTACHONI LANGUAGE JESUS FILM 🎥 .. Invitation to know Jesus #jesusfilmproject @jesusfilm
▶︎

OLUTACHONI LANGUAGE JESUS FILM 🎥 .. Invitation to know Jesus #jesusfilmproject @jesusfilm

MSONKHANO WA CHITSITSIMUTSO
▶︎

MSONKHANO WA CHITSITSIMUTSO

RWANDA: The Country That Rebuilt Itself in 30 Years | 4K Travel Documentary
▶︎

RWANDA: The Country That Rebuilt Itself in 30 Years | 4K Travel Documentary

ថ្ងៃព្រះយេស៊ូវមានព្រះជន្មរស់ឡើងវិញ ( Jesus' Resurrection ) » ឯកសាររឿង
▶︎

ថ្ងៃព្រះយេស៊ូវមានព្រះជន្មរស់ឡើងវិញ ( Jesus' Resurrection ) » ឯកសាររឿង

Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luka 1-2: Kubadwa kwa Yohane Mbatizi-Kubadwa kwa Yesu Khristu
▶︎

Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luka 1-2: Kubadwa kwa Yohane Mbatizi-Kubadwa kwa Yesu Khristu

The Entebbe Raid - Forgotten History
▶︎

The Entebbe Raid - Forgotten History

Greatest SDA Hymns Faith & Worship Vol. 3 | Peaceful Adventist Worship (40 Minutes)
▶︎

Greatest SDA Hymns Faith & Worship Vol. 3 | Peaceful Adventist Worship (40 Minutes)

Moses and the Pharaoh’s Fury (Full Movie 2026) | 4K Biblical Movie
▶︎

Moses and the Pharaoh’s Fury (Full Movie 2026) | 4K Biblical Movie

Chichewa | Machitidwe a Atumwi | NTC.12-19:Uthenga wabwino unayamba kufalikira padziko lonse lapansi
▶︎

Chichewa | Machitidwe a Atumwi | NTC.12-19:Uthenga wabwino unayamba kufalikira padziko lonse lapansi

MSONKHANO WA CHITSITSIMUTSO
▶︎

MSONKHANO WA CHITSITSIMUTSO

The Life of Jesus | English | Official Full HD Movie
▶︎

The Life of Jesus | English | Official Full HD Movie

Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luka 22-24: Imfa ndi Kuuka kwa Yesu Khristu
▶︎

Chichewa movie: Moyo wa Yesu Khristu | Luka 22-24: Imfa ndi Kuuka kwa Yesu Khristu

Жизнь Иисуса по Евангелию от Иоанна. (Полный фильм)
▶︎

Жизнь Иисуса по Евангелию от Иоанна. (Полный фильм)

Chichewa - Nyanja movie: Moyo wa Yesu Khristu | YOHANE 14-17 | Yesu ndiye njira ya kwa Atate
▶︎

Chichewa - Nyanja movie: Moyo wa Yesu Khristu | YOHANE 14-17 | Yesu ndiye njira ya kwa Atate

BARARENDEZA Augustin: A TRIAL IN PRAYER || "WHY WE SHOULD PRAY".
▶︎

BARARENDEZA Augustin: A TRIAL IN PRAYER || "WHY WE SHOULD PRAY".

သခင္ေယ႐ႈသက္ေတာ္စဥ္
▶︎

သခင္ေယ႐ႈသက္ေတာ္စဥ္

=SINZIRA NEZA WUMVA IJAMBO RY'IMANA  ------- INYIGISHO YA Past Antoine RUTAYISIRE
▶︎

=SINZIRA NEZA WUMVA IJAMBO RY'IMANA ------- INYIGISHO YA Past Antoine RUTAYISIRE

Адам и Ева: Истинската история на Сътворението и Изгнанието | ЦЕЛИЯТ ФИЛМ в 4K
▶︎

Адам и Ева: Истинската история на Сътворението и Изгнанието | ЦЕЛИЯТ ФИЛМ в 4K