Troy Mob - Magetsi Azima (Official Music Video)

Music video by Troy Mob performing Magetsi Azima (Official Music Video). 2025 MOB Sound, distributed under Paradise Music Company & SIG Media. Stream "Magetsi Azima" here: Follow Troy Mob:   / troymob285     / troymob.285     / troymob_285   #TroyMob #MagetsiAzima #OfficialMusicVideo Directed by: Popcorn World Co-Directed by: Dir. Raw Shot by: Dir. Raw Starring: Troy Mob, Raffick, The Prince & Tee Video FX & Graphic Design: Popcorn World Lighting: Kelveen Hakim Special Thanks: Paradise Music Company & (HO)2 Studios Typography: Popcorn World Music: Fire Imoji Studios Lyrics: Kenny run it up Magetsi azima Nane ndipange zothima Ndibwera mochedwa osasunga nsima Ndivaye Paris nkaone ana akuvina Magetsi azima Nane ndipange zothima Ndibwera mochedwa osasunga nsima Ndivaye Paris nkaone ana akuvina Undipeza m'munda nsakulima Ma brandy nkagula pa Ema Kukhala high pa phiri no Kina Khutu la nkazi wako ndine m'matsina Mwana sangandipake ine mimba Ndungotchukabe ngati Gijima Kunamizira ngati satimva Koma sangabayite ndi Sativa N'funa ngati chi Vanessa Dimasi Chizivalako anga ma slippers Tisakwiye ndayin'galura sibasi Akhale oti sanadyeko T-kas Ndungodabwa nazo zuchitikazi Angopenga ndi trapper kuchikazi Malaya alije mbwe ma set mayne Fashion killer akuvala tetema Pa ground pa man pachema Chamba chotsala chonse nde tabema Tungozimva udolo nde tabeba Sangavunge beef ali ndi matemba Kuyimba ngati ndili ndi matenda Osakwiya nkazi wako tikatenga Amangofuna yama nails ndi carpenter Iwe umapala banja la ma carpenter Gijima Gijima Gijima Ndungotchukabe ngati Gijima Gijima Gijima Gijima Ndungotchukabe ngati Gijima Magetsi azima Nane ndipange zothima Ndibwera mochedwa osasunga nsima Ndivaye Paris nkaone ana akuvina Magetsi azima Nane ndipange zothima Ndibwera mochedwa osasunga nsima Ndivaye Paris nkaone ana akuvina