Moyo watsopano

“Choncho, tsopano amene ali mwa Khristu Yesu alibe mlandu owatsutsa chifukwa mwa Khristu Yesu, lamulo la Mzimu Woyera amene amapereka moyo, lawamasula ku lamulo la tchimo ndi la imfa. Pakuti zimene Malamulo sanathe kuzichita, popeza anali ofowoka chifukwa cha khalidwe lathu la uchimo, Mulungu anazichita potumiza Mwana wake mʼchifanizo cha munthu ochimwa kuti akhale nsembe yauchimo. Ndipo Iye anagonjetsa tchimo mʼthupi la munthu, ndi cholinga chakuti chilungamo chofunikira cha lamulo chikwaniritsidwe kwathunthu mwa ife amene sitikhala monga mwachikhalidwe chathu cha uchimo koma mwa Mzimu. Pakuti anthu amene amakhala monga mwa makhalidwe oyipa a thupi amayika malingaliro awo pa zinthu zathupi. Koma amene amakhala monga mwa Mzimu amayika malingaliro awo pa zinthu za Mzimu. Kuyika mtima pa zathupi ndi imfa koma kuyika mtima pa za Mzimu ndi moyo ndi mtendere. Pakuti mtima umene wakhazikika pa zathupi ndi wodana ndi Mulungu. Sunagonjere lamulo la Mulungu ndipo sungathe kutero. Ndipo anthu amene amalamulidwa ndi khalidwe lauchimo sangathe kukondweretsa Mulungu. Koma inu simulamulidwanso ndi khalidwe lanu lauchimo koma ndi Mzimu ngati Mzimu wa Mulungu akhaladi mwa inu. Koma ngati munthu aliyense alibe Mzimu wa Khristu, iyeyu si wa Khristu. Ndipo ngati Khristu ali mwa inu, thupi lanu ndi lakufa chifukwa cha uchimo, koma mzimu wanu ndi wamoyo chifukwa cha chilungamo. Ndipo ngati Mzimu wa Mulungu amene anaukitsa Yesu kwa akufa akhala mwa inu, Iyeyo amene anaukitsa Khristu kwa akufa adzapatsanso moyo matupi anu amene amafa kudzera mwa Mzimu wake amene amakhala mwa inu." Aroma‬ ‭8:1-11‬.

254 DIOS TE DICE HOY: LA FE TE MOSTRARÁ LO QUE LA RAZÓN NO PUEDE, Y TE GUIARÁ HACIA LO IMPOSIBLE
▶︎

254 DIOS TE DICE HOY: LA FE TE MOSTRARÁ LO QUE LA RAZÓN NO PUEDE, Y TE GUIARÁ HACIA LO IMPOSIBLE

Galamukani!
▶︎

Galamukani!

Instrumental Worship Guitar : Best Worship Song | Peaceful, Relaxing Instrumental Hymns on Guitar
▶︎

Instrumental Worship Guitar : Best Worship Song | Peaceful, Relaxing Instrumental Hymns on Guitar

28-06-26 Chupehra Sahib Live \ Dhan Dhan Baba Deep Singh Ji | Chuphera Sahib Full Path #wmk
▶︎

28-06-26 Chupehra Sahib Live \ Dhan Dhan Baba Deep Singh Ji | Chuphera Sahib Full Path #wmk

Santo Rosário | Sexta-feira | 04:00 | 26/06/2026 | Live Ao vivo
▶︎

Santo Rosário | Sexta-feira | 04:00 | 26/06/2026 | Live Ao vivo

SPECIAL SUNDAY SERVICE 28TH JUNE 2026
▶︎

SPECIAL SUNDAY SERVICE 28TH JUNE 2026

200 Days - [HARDCORE BEDROCK MINECRAFT]
▶︎

200 Days - [HARDCORE BEDROCK MINECRAFT]

The MAN who changed FOOTBALL forever | Pelé | Documentary
▶︎

The MAN who changed FOOTBALL forever | Pelé | Documentary

Fall Asleep Instantly in 3 Minutes with Heavy Rain | Rain Sounds & Distant Thunder for Deep Sleep
▶︎

Fall Asleep Instantly in 3 Minutes with Heavy Rain | Rain Sounds & Distant Thunder for Deep Sleep

RESTORING THE ORDER 2026 - DAY-7 #dunsinoyekan #worship #intimacy
▶︎

RESTORING THE ORDER 2026 - DAY-7 #dunsinoyekan #worship #intimacy

EILMELDUNG: Sie haben mich ins Visier genommen
▶︎

EILMELDUNG: Sie haben mich ins Visier genommen

Santo Rosário | Sexta-feira | 04:00 | 12/06/2026 | Live Ao vivo
▶︎

Santo Rosário | Sexta-feira | 04:00 | 12/06/2026 | Live Ao vivo

فاهم 36 | سلسلة تذوق العبادات - (1) الصلاة | مع د. أحمد العربي
▶︎

فاهم 36 | سلسلة تذوق العبادات - (1) الصلاة | مع د. أحمد العربي

Destroying A World That Doesn't Exist
▶︎

Destroying A World That Doesn't Exist

Warm Piano Jazz by the Fireplace | Gentle Jazz with Peaceful Lakeview for Work, Study, Focus
▶︎

Warm Piano Jazz by the Fireplace | Gentle Jazz with Peaceful Lakeview for Work, Study, Focus

Way Maker, Best Worship Songs 2026 Collection, Christian Music Album, Hillsong Worship Nonstop
▶︎

Way Maker, Best Worship Songs 2026 Collection, Christian Music Album, Hillsong Worship Nonstop

Rymanowski, Miller: UPA-dek przyjaźni?
▶︎

Rymanowski, Miller: UPA-dek przyjaźni?

How to Actually Build Mobile Apps with AI in 2026 | A Complete Beginner's Tutorial
▶︎

How to Actually Build Mobile Apps with AI in 2026 | A Complete Beginner's Tutorial

BARN FIND Pontiac Grand Prix Forgotten For 25 YEARS! Will It RUN AND DRIVE HOME?
▶︎

BARN FIND Pontiac Grand Prix Forgotten For 25 YEARS! Will It RUN AND DRIVE HOME?

Relaxing Rain Sounds and Soft Piano Music for Deep Sleep, Stress Relief, and Peaceful Nights
▶︎

Relaxing Rain Sounds and Soft Piano Music for Deep Sleep, Stress Relief, and Peaceful Nights