Ndege Za Shepherd Bushiri Ndi Chuma China Chodabwisa Zinapita Kuti ?
NDEGE ZA BUSHIRI ZINAPITA KUTI? A Shepherd Bushiri ndi mtsogoleri komanso mwini wa mpingo wina omwe umadziwika ndi dzina loti Enlightened Christian Gathering (ECG). Kamba kakupanga zinthu zozizwitsa ndi zodabwitsa pa moyo wawo wolalika komanso ndi moyo wawo wokonda zinthu zodula zomwe zambiri ndi zapamwamba kwambiir, anthu ambiri amawadziwa makamaka chigawo chino cha Africa. Iwo ndi mwana wa Prophet Uebert Angel mu uzimu (spiritual son) yemwe amakhala mdziko la United Kingdom (UK) ndipo zimamveka kuti ndi mmodzi mwa anthu olalika omwe ndi olemera kwambiri muno mu dera la Africa. Kuyambira mchaka cha 2015, a Bushiri akhala akukumana ndi zinthu zomwe zakhala zikuwoneka kuti zikhoza kusokoneza utumiki wawo koma pa 1 February mu chaka cha 2019, iwo pamodzi ndi mkazi wawo Mary yemwe amatinso ndi mneneri ngati amuna awo, anamangidwa.

NI NDE WATEKEREZAGA KO IRAN YAMARA IKI GIHE CYOSE MU NTAMBARA? // KNC NA MUTABARUKA

GOtv Malawi Izeki ndi Jakobo Safunsa anadya phula

WILD AMAZON | When Survival is in the Hands of Predators | Nature Animal Documentary

Tionge Chimbalanga (Aunt Tiwo) Uncensored chat with Raphael Moses

ZIFUKWA ZANGA NZOKWANILA VIDEO

The war on Iran showed limits of America's power abroad | Vali Nasr | The David Hearst Podcast

The Clement Manyathela Show | LIVE

The NdB Sunday Show: Bring down SA’s “Political Ponzi Scheme”! | with Solly Moeng

TIKUFERANJI 25 MAY 2019

She Sold Fish to Make Him a Lawyer... He Sued Her for Divorce.

Zaululika Chilungamo Pakuthawa Kwa Prophet Shepherd Bushiri Ndi Mary Mdziko La South Africa

PROPHET SHEPHERD BUSHRI HONOURED IN HIS HOMELAND

ZAULULIKA CHILIMA ANKADZIWA KUTI APHEDWA PA NGOZI YA NDEGE

702 Breakfast with Bongani Bingwa | LIVE

Chenjerai akandotora sandawana kuti aite mari fast fast/ Prophet Miracle Paul

Muchapera kufa musha wese kana mukasanamata/ Prophet Miracle Paul

Sithole Ozarura Huru muDare Hakuna Secret Yasiiwa. Oti Mukoma Ari Kurwara Arikufa - Saunyama (Prt 4)

Chuma Chose Cha Prophet Shepherd Bushiri

Izeki ndi Jacob Live on MBC

