Team yomwe itenge AIRTEL TOP 8 mosavutikila

Ma quarter finals oyamba mu mpikisano wa Airtel Top 8 atha mokomela ma team a Mighty Wanderers ndi Silver Strikers. Koma pali ma mistake angapo omwe ma team anachita omwe apangitsa kuti masewero ena athe musawakomela. Katswiri pa nkhani za mpira mdziko muno Wesyslyas Chirwa wapeleka maganizo ake. #kickoffmalawi #fcbnyasabigbullets #mightywanderers #silverstrikers #Airteltop8