John Chilembwe Documentary
Patha zaka 110 kuchokera pomwe m’busa John Chilembwe adaphedwa m’chaka cha 1915 akumenya nkhondo yolimbana ndi atsamunda. Pomwe pa 15 January chaka ndi chaka aMalawi amakumbukira Chilembwe, papezeka mbali ziwiri zomwe zikunena kuti ndiwo mbumba yeniyeni ya Chilembwe. Gulu lina ndi la m’midzi ya Mpelule ndi Chikapa kwa T/A Chikowi ku Zomba. Pomwe lina ndi la m’mudzi mwa Mkwaila, T/A Kadewere ku Chiradzulu. Wonerani kanemuyu kuti mumve zambiri.

▶︎
DOCUMENTARY ON BAKILI MULLUZI

▶︎
Times Investigation on Silombera - 5 February 2021

▶︎
THE GUNLESS SOLDIER FULL FILM

▶︎
Nyadzonya Revenge, Ngozi YaChief Makoni's White Wife, Jerenyenje Special Branch, Cde Rex Mapfumo

▶︎
Trap squad-John Chilembwe REMIXOfficial HD video

▶︎
Times Investigation 1967 Mwanza war - 20 February 2022

▶︎
EP 9| MWANZA MURDER | THAMBANI | NDALE M'MBUYOMO| MZATI TV

▶︎
KUFUKULA MBIRI YA MARCUS GARVEY| MZATI TV

▶︎
CRUISE 5 WITH BYSON KAULA - DEATH ROW SURVIVOR

▶︎
TIKUFERANJI 01 JULY 2017

▶︎
Walter Nyamilandu Manda - From Football to Politics | Ep 027 | Face2Face Podcast

▶︎
Times Investigation featuring Simba Nkwinda – 20 October 2024

▶︎
LIVE: KUFUKULA MBIRI YA SAMORA MACHEL-MZATI TV

▶︎
WaGanyu EXCLUSIVE INTERVIEW WITH YAMIKANI CHESTER

▶︎
Kufukula Mbiri ya John Chilembwe Part 2 on Mzati TV

▶︎
Why Mobutu Kept the Corpse of a Foreign President in His House For 3 Years

▶︎
POLICE KUMUKALIPIRA KUNKUYU | AKANADZIWA MOSES SAKANAPANGA IZI #moseskunkuyu #breakingnews #viral

▶︎
#CoupDeterred: Intrigues of 1982 attempted coup on President Moi's government

▶︎
CRUISE 5 WITH PHUNGU JOSEPH NKASA 17th OCTOBER 2021

▶︎
