Anamusungunula mu acid atawamenyera ufulu | Nkhani ya Patrice Lumumba

Atamenyera ufulu wa dziko lake la Decocrating Republic of Congo, Patrice Lumumba anapangidwa chiwembu ndi anzake omwe iye anawakweza mma udindo. Iyi mdi nkhani ya kuphedwa kwa Prime Minister Oyamba wa ku DRC mu 1961. #malawi #nkhani #malawian #africanhistory