Madyedwe Hour Live

Thom Kamanga a kucheza ndi nkulu wa sukulu ya luso la kusoka ya EMINENCE TAILORING SCHOOL a Frackson Pangani kucheza zokhuza ndondomeko yozindikira luso la munthu ndi kumpatsa Certificate ya Boma