Nyasa Files | Sexual harassment| 16 May 2026
Sexual harassment ndi nkhani yeniyeni yomwe ikukhudza anthu ambiri ku ntchito, kusukulu, m’mabizinesi, komanso m’madera athu. Mu video iyi tikufotokoza tanthauzo la sexual harassment, momwe imachitikira, zitsanzo zake, komanso momwe tingatetezere anthu ku nkhanza zoterezi. Munthu aliyense ayenera kulemekezedwa. Mawu onyansa, kukhudza munthu mosafunikira, ma joke a kugonana, ma message osayenera, kapena kukakamiza munthu pa nkhani za kugonana si bwino. Tiyeni tipange malo otetezeka komanso aulemu kwa aliyense. 🔹 Phunzirani 🔹 Dziwitsani ena 🔹 Limbani ndi nkhanza 🔹 Lemekezani anthu #SexualHarassment #LekaniNkhanza #Respect #Malawi #Awareness #StopAbuse #Chichewa #WorkplaceEthics

▶︎
90+ Sports Show - 15 June 2026

▶︎
Chief Mutasa - Sabhuku Oti Zvamataura Mambo Handisi Kuzozviita. Hazvina Kupera Mushe (Part 1)

▶︎
BMTv

▶︎
Nyasa Files EP01 - Defilement - May 9, 2026

▶︎
MY LANDLORD OVERSTEPPED HIS BOUNDARIES || Justice Court EP 285

▶︎
IWOPENI WANDERERS! Ma tactics a Bob Mpinganjira akusokoneza ma team watero Katswiri wokamba za mpira

▶︎
The Australia Mystery Nobody Can Explain | The Mysterious Death of Sheila Chebii | Crime Dopers

▶︎
ACHITA KUYIKA PA MBALAMBANDA KUTI CHAKWERA AYALUKE~MAUMBONI AWA APEZEKA

▶︎
From Zim to the UK: She proudly manages her son's flock of 2K Black Australorp Roadrunner chickens

▶︎
I was just trying to survive! Wife confesses to cheating due to poverty in Headman Murape's primary

▶︎
90+ Sports Show - Francis Mkonda Part 2

▶︎
THE OFFICIAL SIDE CHICK:TINASHE MUGABE DNA SHOW S21 EP13

▶︎
90+ Sports Show -12 June 2026

▶︎
Chief Mutasa | Muroja akandipindira ndichigeza

▶︎
ZOMWE WAYANKHURA NJAWALA CHAKWERA AKOMOKA NDI BP~ CHAKWERA ANAPANGIRANJI KOMA

▶︎
The Richest Family in CAMEROON & The Secrets Behind Their Fortune...

▶︎
Invited to a Fresher's Party at Kabarak University, She's Found dead & naked | Murder Tapes SN3 EP5

▶︎
90+ Sports Show

▶︎
South africans now Beg for forgiveness as more African Countries Retaliate over Xenophobic attacks

▶︎
