Sosobina John G Mandanda wapereka mayankho a mafunso anu aja.

🔴#𝗣𝗵𝗮𝗮𝗮!🚩Mathias Masache wa Katomfu media anakacheza ndi Msangalatsi John G Mandanda ku Mulanje. Kanemayu akuonetsa macheza onse omwe mamulumuzana awiriwa anali nawo mkucheza kwawo. Pangani Subscribe komanso kugawa link ya kanemayu kwa amzanu kuti nawonso asangalale nawo ndi Machezawa. #TeamKatomfu #KugayaStuff #malawi #zambia #southafrica